Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Phunzitsani Ana Anu Kukonda Yehova

Phunzitsani Ana Anu Kukonda Yehova

Makolo ayenela kukulitsa cikondi cawo pa Yehova (Deut. 6:5; w05 6/15 20 ¶11)

Ayenela kupeleka citsanzo cabwino kwa ana awo (Deut. 6:6; w07 5/15 15-16)

Ayenela kuphunzitsa ana awo za Yehova kaŵili-kaŵili (Deut. 6:7; w05 6/15 21 ¶14)

Kuwonjezela pa kulambila kwa pabanja, ni mipata ina iti imene mungaphunzitsile ana anu kukonda Yehova na mfundo zake?