Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

June 28–July 4

DEUTERONOMO 9-10

June 28–July 4

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • Kodi Yehova Mulungu Wanu Akufuna Kuti Muzicita Ciani?”: (10 min.)

  • Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)

    • Deut. 9:1-3—Ngakhale kuti ana a Anaki anali “anthu amphamvu ndi aatali,” n’cifukwa ciani Aisiraeli sanafunike kuwaopa? (it-1 103)

    • Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo yopindulitsa iti imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?

  • Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) Deut. 10:1-22 (th phunzilo 10)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 135

  • Maseŵela a pa Vidiyo: Kodi Mukupambanadi?: (Mph. 7) Kukambilana. Onetsani vidiyoyi. Ndiyeno funsani omvetsela mafunso aya: Kodi maseŵela a pa vidiyo angakubweletseleni mavuto otani? Ni zinthu ziti pa umoyo zimene n’zofunika kwambili kuposa maseŵela a pa vidiyo? (Aef. 5:15, 16) Kodi maseŵela a pa vidiyo amene mumasankha amaonetsa bwanji umunthu wanu wam’kati? Kodi mungacite ciani kuti mukhaledi wopambana pa umoyo?

  • “Muzipanga Zosankha Mwanzelu Pankhani ya Moŵa”: (Mph. 8) Kukambilana. Onetsani vidiyo yakuti Ganizilani Zotulukapo za Kumwa Moŵa.

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) lfb phunzilo 43

  • Mawu Othela (Mph. 3)

  • Nyimbo 44 na Pemphelo