Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Malamulo a Yehova ni Anzelu Komanso Olungama

Malamulo a Yehova ni Anzelu Komanso Olungama

Timaonetsa nzelu na kuzindikila ngati timvela malamulo a Mulungu (Deut. 4:6; it-2 1140 ¶5)

Ambili akaona zocita zathu amazindikila kuti malamulo a Mulungu ni anzelu (Deut. 4:6; w99 11/1 20 ¶6-7)

Anthu a Yehova ali na umoyo wabwino kwambili kuposa anthu ena (Deut. 4:7, 8; w07 8/1 29 ¶13)

Anthu ambili amabwela m’gulu la Yehova akaona makhalidwe abwino a anthu amene amatsatila malamulo a Mulungu na mfundo zake.

Ni madalitso otani amene mwapeza cifukwa cotsatila malangizo a Yehova anzelu?