Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

May 10-16

NUMERI 30–31

May 10-16

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • Muzikwanilitsa Malumbilo Anu”: (Mph. 10)

  • Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)

    • Num. 30:10-12—Tidziŵa bwanji kuti Elikana anavomeleza lumbilo la Hana lakuti adzapeleka Samueli kwa Yehova kuti azikam’tumikila? (it-2 28 ¶1)

    • Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo yopindulitsa iti imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?

  • Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) Num. 30:1-16 (th phunzilo 5)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 5

  • Zolengedwa Zimatiphunzitsa Kupilila: (Mph. 15) Kukambilana. Onetsani vidiyoyi. Ndiyeno funsani mafunso otsatilawa pa comela, nyama, na couluka ciliconse cimene cili mu vidiyoyi: Kodi colengedwa cimeneci citiphunzitsa ciani pa nkhani ya kupilila? Tingaonetse bwanji kupilila kotelo mu umoyo wathu monga Akhristu?

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) lfb phunzilo 36

  • Mawu Othela (Mph. 3)

  • Nyimbo 50 na Pemphelo