Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

May 17-23

NUMERI 32–33

May 17-23

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • Mukapitikitse Anthu Onse a m’Dzikolo”: (Mph. 10)

  • Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)

    • Num. 33:54—Kodi malo anali kugaŵidwa bwanji ku mafuko a Isiraeli? (it-1 359 ¶2)

    • Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo yopindulitsa iti imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?

  • Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) Num. 32:28-42 (th phunzilo 5)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

UMOYO WATHU WACIKHRISTU