Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

June 6-12

2 SAMUELI 9-10

June 6-12

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • Davide Anaonetsa Cikondi Cosasintha”: (Mph. 10)

  • Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)

    • 2 Sam. 10:4, 5—N’cifukwa ciyani zimene anacita Hanuni kunali kuwanyoza amuna aciisiraeli? (it-1 266)

    • Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo yopindulitsa iti imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?

  • Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) 2 Sam. 9:1-13 (th phunzilo 12)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 116

  • Kumbukilani Mmene Cikondi Cilili—N’cokoma Mtima: (Mph. 5) Kukambilana. Tambitsani vidiyoyi. Kenako, funsani omvetsela mafunso awa: Kodi Davide anam’komela mtima motani Mefiboseti? Kodi tingawaonetse bwanji ena kukoma mtima komanso cikondi cosasintha?

  • Zimene Gulu Lakwanitsa Kucita: (Mph. 10) Onetsani vidiyo yakuti Zimene Gulu Lakwanitsa Kucita ya June.

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) lff phunzilo 07

  • Mawu Othela (Mph. 3)

  • Nyimbo 1 na Pemphelo