Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Tiphunzilapo Ciyani pa Nyimbo Yochedwa “Uta”?

Tiphunzilapo Ciyani pa Nyimbo Yochedwa “Uta”?

[Onetsani vidiyo yakuti Mfundo Zokhudza Buku la 2 Samueli.]

Onetsani ulemu kwa amene ali na ulamulilo (2 Sam. 1:17, 18, 23, 24; w00 6/15 13 ¶9)

Onetsani kuti ndinu okhulupilika kwa mabwenzi anu (2 Sam. 1:25, 26; w12 4/15 10 ¶8)

DZIFUNSENI KUTI: ‘Kodi ningaonetse bwanji kuti nimalemekeza akulu mumpingo? Ningaonetse bwanji kuti ndine wokhulupilika kwa Akhristu anzanga?’