Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

May 2-8

1 SAMUELI 27-29

May 2-8

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • Mapulani a Davide a Kamenyedwe ka Nkhondo”: (Mph. 10)

  • Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)

    • 1 Sam. 28:15—Kodi Sauli “anaona” ndani pa cocitikaci? (w10 1/1 20 ¶5-6)

    • Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo yopindulitsa iti imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?

  • Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) 1 Sam. 27:1-12 (th phunzilo 5)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 129

  • Analimbabe pa Cizunzo: (Mph. 15) Kukambilana. Tambitsani vidiyoyi. Ndiyeno, funsani omvetsela mafunso awa: Kodi tiphunzilapo ciyani pa citsanzo ca abale athu pa nthawi ya ulamulilo wa Nazi ku Germany? Tiphunzilapo ciyani pa citsanzo ca abale athu a ku Russia, komanso a m’nthawi ya ulamulilo wakale wa Soviet Union?

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) lff phunzilo 02

  • Mawu Othela (Mph. 3)

  • Nyimbo 94 na Pemphelo