Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Khalanibe na Mantha Oyenela Oopa Kukhumudwitsa Yehova

Khalanibe na Mantha Oyenela Oopa Kukhumudwitsa Yehova

Kukhala na zolinga zabwino si cifukwa cophwanyila malamulo a Yehova (2 Sam. 6:3-5; w05 5/15 17 ¶8)

Uza anaphwanya lamulo la Mulungu (2 Sam. 6:6; w05 2/1 27 ¶20)

Yehova analanga Uza cifukwa cocita cinthu cosalemekeza Mulungu (2 Sam. 6:7; w05 2/1 27 ¶21)

DZIFUNSENI KUTI, ‘Pa umoyo wanga, ningaonetse bwanji kuti nimaopa kukhumudwitsa Yehova?’—Miy. 3:7