Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Dzilimbitseni mwa Yehova Mulungu Wanu

Dzilimbitseni mwa Yehova Mulungu Wanu

Aamaleki anatentha mzinda wa Zikilaga n’kutenga anthu a mumzindawo kuti akakhale akapolo awo (1 Sam. 30:1, 2)

Davide na amuna amene anali naye anavutika kwambili maganizo (1 Sam 30:3-5; w06 8/1 28 ¶12)

Davide anapeza mphamvu mwa Yehova (1 Sam. 30:6; w12 4/15 30 ¶14)

ZOYENELA KUZIGANIZILA: Nikapanikizika maganizo, kodi nimapeza mphamvu kwa ndani?