June 12-18
2 MBIRI 32-33
Nyimbo 103 na Pemphelo
Mawu Oyamba (Mph. 1)
CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Muzilimbikitsa Ena pa Nthawi Zovuta”: (Mph. 10)
Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)
2 Mbiri 33:15, 16—Kodi tiphunzilapo ciyani pa citsanzo ca Manase? (w21.10 4-5 ¶11-12)
Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo iti yokupindulilani imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?
Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) 2 Mbiri 32:1-15 (th phunzilo 11)
CITANI KHAMA PA ULALIKI
Ulendo Woyamba: (Mph. 4) Kambilanani mfundo za pacikuto ca kumbuyo ca bulosha yakuti Kondwelani na Moyo Kwamuyaya!, na kumupempha kuti muyambe kuphunzila naye Baibo. (th phunzilo 6)
Ulendo Wobwelelako: (Mph. 3) Makambilano anu atsamile pa mfundo yaikulu ya makambilano acitsanzo. M’gaŵileni cofalitsa ca m’Thuboksi yathu. (th phunzilo 17)
Phunzilo la Baibo: (Mph. 5) lff phunzilo 10 mfundo 5 (th phunzilo 19)
UMOYO WATHU WACIKHRISTU
“Dziteteni kwa Anthu Ampatuko”: (Mph. 10) Kukambilana komanso kuonelela vidiyo.
Zofunikila za Mpingo: (Mph. 5)
Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) lff phunzilo 48 mfundo 1-4
Mawu Othela (Mph. 3)
Nyimbo 90 na Pemphelo