June 26–July 2
EZARA 1-3
Nyimbo 75 na Pemphelo
Mawu Oyamba (Mph. 1)
CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Lolani Kuti Yehova Akugwilitseni Nchito”: (Mph. 10)
Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)
Ezara 1:5, 6—Kodi tiphunzilapo ciyani kwa Aisiraeli ena amene anatsala ku Babulo? (w06 1/15 19 ¶1)
Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo iti yokupindulilani imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?
Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) Ezara 2:58-70 (th phunzilo 5)
CITANI KHAMA PA ULALIKI
Ulendo Woyamba: (Mph. 3) Makambilano anu atsamile pa mfundo yaikulu ya makambilano acitsanzo. Mukayamba, mwininyumba akambe mawu ofala kwanuko ofuna kukanila ulaliki. Koma mwaluso loŵelani pa mawu amenewo. (th phunzilo 3)
Ulendo Wobwelelako: (Mph. 4) Makambilano anu atsamile pa mfundo yaikulu ya makambilano acitsanzo. Ndiyeno m’gaŵileni bulosha yakuti Kondwelani na Moyo Kwamuyaya! (th phunzilo 9)
Phunzilo la Baibo: (Mph. 5) lff phunzilo 10 cidule cake, mafunso obweleza, komanso colinga (th phunzilo 8)
UMOYO WATHU WACIKHRISTU
“Pezani Cimwemwe Poyambitsa Makambilano”: (Mph. 15) Kukambilana komanso kutamba vidiyo.
Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) lff phunzilo 49 mfundo 1-5
Mawu Othela (Mph. 3)
Nyimbo 132 na Pemphelo