Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Lolani Kuti Yehova Akugwilitseni Nchito

Lolani Kuti Yehova Akugwilitseni Nchito

[Onetsani vidiyo yakuti Mfundo Zokhudza Buku la Ezara.]

Yehova analimbikitsa mtima wa Mfumu Koresi kuti amasule Aisiraeli mu ukapolo (Ezara 1:1-3; w22.03 14 ¶1)

Yehova analimbikitsa mitima ya anthu ake kuti akamangenso kacisi (Ezara 1:5; w17.10 26 ¶2)

Ngati ndinu wodzipeleka, Yehova angakupangitseni kukhala ciliconse cimene afuna kuti akwanilitse cifunilo cake.