Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

June 5-11

2 MBIRI 30–31

June 5-11

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • Kusonkhana Pamodzi Kumatipindulila”: (Mph. 10)

  • Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)

    • 2 Mbiri 30:20—Tiphunzilapo ciyani tikaganizila mmene Yehova anayankhila pemphelo la Hezekiya? (w18.09 6 ¶14-15)

    • Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo iti yokupindulilani imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?

  • Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) 2 Mbiri 31:11-21 (th phunzilo 5)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 74

  • Khala Bwenzi la Yehova—Konzekela Yankho Lako: (Mph. 5) Kukambilana. Onetsani vidiyoyi. Ndiyeno ngati n’zotheka, funsani acicepele m’gulu mafunso awa: Kodi mungakonzekele bwanji kuti mukapelekepo ndemanga pa msonkhano? N’cifukwa ciyani tingakhalebe acimwemwe ngakhale kuti sanatipatseko mwayi wopelekapo ndemanga?

  • Zimene Gulu Lakwanitsa Kucita: (Mph. 10) Onetsani vidiyo ya Zimene Gulu Lakwanitsa kucita ya June.

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) lff mafunso obweleza a cigawo 3

  • Mawu Othela (Mph. 3)

  • Nyimbo 115 na Pemphelo