Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Kusonkhana Pamodzi Kumatipindulila

Kusonkhana Pamodzi Kumatipindulila

Hezekiya anakonza phwando lalikulu pa Pasika ku Yerusalemu (2 Mbiri 30:1;it-1 1103 ¶2)

Anthu ambili anapezekapo ngakhale kuti panali otsutsa (2 Mbiri 30:10, 11, 13; it-1 1103 ¶3)

Iwo anasangalala kwambili ndipo analimbikitsidwa kutumikila Yehova (2 Mbiri 25–31:1; it-1 1103 ¶4-5)

DZIFUNSENI KUTI: ‘Kodi napindula bwanji cifukwa copezeka pa misonkhano yampingo komanso ikuluikulu ya pamaso-m’pamaso?’