May 1-7
2 MBIRI 17–19
Nyimbo 114 na Pemphelo
Mawu Oyamba (Mph. 1)
CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Muziona Ena Mmene Yehova Amawaonela”: (Mph. 10)
Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)
2 Mbiri 17:9—Kodi tingaphunzilepo ciyani pa nchito yophunzitsa anthu imene Yehosafati anayambitsa? (w17.03 20 ¶10-11)
Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo iti yokupindulilani imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?
Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) 2 Mbiri 17:1-19 (th phunzilo 11)
CITANI KHAMA PA ULALIKI
Vidiyo ya Ulendo Woyamba: (Mph. 5) Kukambilana. Onetsani vidiyo yakuti Ulendo Woyamba: Baibo—Aroma 15:4. Nthawi zonse vidiyo ikaima, inunso iimitseni na kufunsa omvela mafunso amene aonekela.
Ulendo Woyamba: (Mph. 3) Makambilano anu atsamile pa mfundo yaikulu ya makambilano acitsanzo. (th phunzilo 18)
Nkhani: (Mph. 5) w21.05 17-18 ¶11-15 —Mutu: Khalanibe na Maganizo Oyenela Ngati Anthu Alibe Cidwi. (th phunzilo 16)
UMOYO WATHU WACIKHRISTU
“Muzidziona Mmene Yehova Amakuonelani”: (Mph. 15) Kukambilana na kutamba vidiyo.
Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) lff phunzilo 44 mfundo 5-6, cidule cake, mafunso obweleza, komanso colinga
Mawu Othela (Mph. 3)
Nyimbo 111 na Pemphelo