May 15-21
2 MBIRI 22-24
Nyimbo 73 na Pemphelo
Mawu Oyamba (Mph. 1)
CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Yehova Amadalitsa Anthu Ocita Zinthu Molimba Mtima”: (Mph. 10)
Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)
2 Mbiri 24:22—Kodi ulosi wa Zekariya unakwanilitsika bwanji? (it-2 1223 ¶13)
Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo iti yokupindulilani imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?
Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) 2 Mbiri 22:1-12 (th phunzilo 5)
CITANI KHAMA PA ULALIKI
Ulendo Woyamba: (Mph. 3) Makambilano anu atsamile pa mfundo yaikulu ya makambilano acitsanzo. M’gaŵileni cofalitsa ca m’Thuboksi yathu. (th phunzilo 1)
Ulendo Wobwelelako: (Mph. 4) Makambilano anu atsamile pa mfundo yaikulu ya makambilano acitsanzo. Muitanileni ku misonkhano. (th phunzilo 17)
Nkhani: (Mph. 5) w10 2/15 6-8 ¶6-10—Mutu: Mzimu wa Yehova Udzakuthandizani Kukhala Wolimba Mtima. (th phunzilo 8)
UMOYO WATHU WACIKHRISTU
Zofunikila za Mpingo: (Mph. 15)
Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) lff phunzilo 45 mfundo 4 komanso cidule cake, mafunso obweleza, na colinga
Mawu Othela (Mph. 3)
Nyimbo 37 na Pemphelo