Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Yehova Amadalitsa Anthu Ocita Zinthu Molimba Mtima

Yehova Amadalitsa Anthu Ocita Zinthu Molimba Mtima

Yehosabati na mwamuna wake Yehoyada, anateteza Yehoasi kwa Ataliya. (2 Mbiri 22:11, 12; w09 4/1 24 ¶1-2)

Molimba mtima, Yehoyada anaika Yehoasi kukhala mfumu (2 Mbiri 23:1-11, 14, 15; w09 4/1 24 ¶3-5)

Yehoyada atamwalila anapatsidwa ulemu wapadela woikidwa m’manda a mafumu (2 Mbiri 24:15, 16; it-1 379 ¶5)

ZOYENELA KUSINKHASINKHA: Ni pa mbali ziti za kulambila kwathu pamene niyenela kuonetsa kulimba mtima kwambili?