Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

May 22-28

2 MBIRI 25–27

May 22-28

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Yehova Akhoza Kukupatsani Zambili Kuposa Pamenepa”: (Mph. 10)

  • Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)

    • 2 Mbiri 26:4, 5—Tiphunzilapo ciyani pa citsanzo ca Uziya za kufunika kokhala na m’bale kapena mlongo wokhwima kuuzimu, amene angatithandize kupanga zisankho mwanzelu? (w07 12/15 10 ¶1-2)

    • Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo iti yokupindulilani imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?

  • Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) 2 Mbiri 25:1-13 (th phunzilo 12)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 136

  • Khalani Wokonzeka Kudzimana Ciliconse Kuti Mukapeze Moyo Wosatha (Maliko 10:29, 30): (Mph. 15) Kukambilana. Onetsani vidiyoyi. Kenako funsani omvela mafunso aya: Kodi lonjezo la Yesu la pa Maliko 10:29, 30 liyenela kutilimbikitsa kucita ciyani? Kodi Yesu anamvela bwanji pamene abale ake sanamukhulupilile poyamba? Tiyenela kukumbukila ciyani za a m’banja lathu amene si Mboni?

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) lff phunzilo 46

  • Mawu Othela (Mph. 3)

  • Nyimbo 51 na Pemphelo