Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

“Yehova Akhoza Kukupatsani Zambili Kuposa Pamenepa”

“Yehova Akhoza Kukupatsani Zambili Kuposa Pamenepa”

Amaziya analemba ganyu asilikali kuti akamuthandize polimbana na adani a Mulungu (2 Mbiri 25:5, 6)

Munthu wa Mulungu anauza Amaziya kuti awabweze asilikaliwo (2 Mbiri 25:7, 8; it-1 1266 ¶6)

Yehova akanamupatsa zambili Amaziya kuposa ndalama zimene anataya (2 Mbiri 25:9, 10)

DZIFUNSENI KUTI: ‘Kodi ningadzimane zinthu ziti kuti nicite zambili potumikila Yehova? Nanga ningapeze madalitso otani nikacita zimenezo?’—Mal. 3:10; w21.08 30 ¶16