May 29–June 4
2 MBIRI 28–29
Nyimbo 54 na Pemphelo
Mawu Oyamba (Mph. 1)
CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Mungamutumikile Yehova Ngakhale Kuti Makolo anu Sanapeleke Citsanzo Cabwino”: (Mph. 10)
Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)
2 Mbiri 29:25—Kodi citsanzo ca Natani citiphunzitsa ciyani za madalitso amene timapeza tikalola Yehova kutiwongolela? (w12 2/15 24-25)
Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo iti yokupindulilani imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?
Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) 2 Mbiri 28:1-11 (th phunzilo 10)
CITANI KHAMA PA ULALIKI
Ulendo Woyamba: (Mph. 3) Makambilano anu atsamile pa mfundo yaikulu ya makambilano acitsanzo. Mukayamba, mwininyumba akambe mawu ofala kwanuko ofuna kukanila ulaliki. Koma mwaluso loŵelani pa mawu amenewo. (th phunzilo 4)
Ulendo Wobwelelako: (Mph. 3) Makambilano anu atsamile pa mfundo yaikulu ya makambilano acitsanzo. M’gaŵileni cofalitsa ca m’Thuboksi yathu. (th phunzilo 19)
Phunzilo la Baibo: (Mph. 6) lff phunzilo 10 mfundo 4 (th phunzilo 13)
UMOYO WATHU WACIKHRISTU
Yehova ni “Tate wa Ana Amasiye”: (Mph. 8) Kukambilana na kutamba vidiyo.
Zofunikila za Mpingo: (Mph. 7)
Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) lff phunzilo 47
Mawu Othela (Mph. 3)
Nyimbo 89 na Pemphelo