Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

May 8-14

2 MBIRI 20–21

May 8-14

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Khulupililani Yehova Mulungu Wanu”: (Mph. 10)

  • Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)

    • 2 Mbiri 21:14, 15—Kodi ulosi wa Eliya wokamba za Yehoramu unakwanilitsika bwanji? (it-1 1271 ¶1-2)

    • Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo iti yokupindulilani imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?

  • Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) 2 Mbiri 20:20-30 (th phunzilo 10)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

UMOYO WATHU WACIKHRISTU