UMOYO NA UTUMIKI WATHU–KABUKU KA MISONKHANO November 2016
Maulaliki a Citsanzo
Maulaliki a citsanzo oseŵenzetsa pogaŵila Nsanja ya Mlonda ndi mfundo ya coonadi ya m’Baibo imene igwilizana na zimene zicitika masiku ano. Seŵenzetsani maulaliki a citsanzo pokonza ulaliki wanu.
CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU
Baibo Imakamba za Mkazi Wabwino
Kodi Yehova amafuna kuti mkazi wokwatiwa akhale na makhalidwe ati?
UMOYO WATHU WACIKHIRISTU
“Mwamuna Wake Amadziŵika Pazipata”
Mkazi wabwino amapeleka cithunzi cabwino ca mwamuna wake.
CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU
Muzikondwela Pogwila Nchito Mwakhama
N’zotheka kukondwela na nchito ngati tikhala na maganizo oyenela.
UMOYO WATHU WACIKHIRISTU
Mmene Tingaseŵenzetsele Buku la Zimene Baibulo Ingatiphunzitse
Tingaseŵenzetse bwanji zinthu zatsopano za m’bukuli pocititsa phunzilo la Baibo?
CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU
“Kumbukila Mlengi Wako Wamkulu Masiku a Unyamata Wako”
Mwa mau a ndakatulo, Mlaliki 12 amalimbikitsa acicepele kuseŵenzetsa bwino mipata imene ali nawo.
UMOYO WATHU WACIKHIRISTU
Acicepele—Musazengeleze Kuloŵa pa ‘Khomo Lalikulu’
Kodi mungadziikile zolinga zauzimu monga kucitako utumiki wa nthawi zonse?
CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU
Mtsikana Wacisulami n’Citsanzo Cabwino Cofunika Kutengela
N’ciani cinam’pangitsa kukhala citsanzo cabwino kwa alambili a Yehova?