Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

November 7-13

MIYAMBO 27-31

November 7-13
  • Nyimbo 86 na Pemphelo

  • Mau Oyamba (Mph. 3 kapena zocepelapo)

CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU

  • Baibo Imakamba za Mkazi Wabwino”: (Mph. 10)

    • Miy 31:10-12—Amakhala wodalilika (w15 1/15, tsa. 20 ndime 10; w00 2/1-CN, tsa. 31 ndime 2; it-2 tsa. 1183)

    • Miy. 31:13-27—Amakhala wakhama pa nchito (w00 2/1-CN, tsa. 31 ndime 3-4)

    • Miy. 31:28-31—Amakhala munthu wauzimu, woyenela kutamandidwa (w15 1/15 tsa. 20 ndime 8; w00 2/1-CN, tsa. 31 ndime 5, 8)

  • Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (Mph. 8)

    • Miy. 27:12—Tingaonetse bwanji kuti ndife ocenjela pamene tisankha zosangulutsa? (w15 7/1 tsa. 8 ndime 3)

    • Miy 27:21—Kodi “citamando copelekedwa kwa munthu cimasonyeza” bwanji “mmene iye alili”? (w11 8/1-CN, tsa. 29 ndime 2; w06 9/15-CN, tsa. 19 ndime 12)

    • Kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno kwaniphunzitsa ciani za Yehova?

    • Ni mfundo ziti pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno zimene ningaseŵenzetse mu ulaliki?

  • Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4 kapena zocepelapo) Miy. 29:11–30:4

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Konzekelani Maulaliki a Mwezi Uno: (Mph. 15) Kukambilana. Tambitsani vidiyo ya citsanzo iliyonse ndi kukambilana zimene mwaphunzilapo. Limbikitsani ofalitsa kukonza ulaliki wawo.

UMOYO WATHU WACIKHIRISTU