November 14-20
MLALIKI 1–6
Nyimbo 66 na Pemphelo
Mau Oyamba (Mph. 3 kapena zocepelapo)
CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU
“Muzikondwela Pogwila Nchito Mwakhama”: (Mph. 10)
[Tambitsani vidiyo yakuti Mfundo Zokhudza Buku la Mlaliki..]
Mlal. 3:12, 13—Cimwemwe cimene timapeza cifukwa cogwila nchito mwakhama ndi mphatso yocokela kwa Mulungu (w15 2/1 tsa. 4-6)
Mlal. 4:6—Muziona nchito moyenela (w15 2/1 tsa. 6 ndime 3-5)
Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (Mph. 8)
Mlal. 2:10, 11—Kodi Solomo anazindikila mfundo yanji pa nkhani ya cuma? (w08 4/15-CN, tsa. 22 ndime 9-10)
Mlal. 3:16, 17—Kodi tiyenela kumvela bwanji na zinthu zopanda cilungamo zimene zimacitika m’dzikoli? (w06 11/1-CN, tsa. 14 ndime 9)
Kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno kwaniphunzitsa ciani za Yehova?
Ni mfundo ziti pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno zimene ningaseŵenzetse mu ulaliki?
Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4 kapena zocepelapo) Mlal. 1:1-18
CITANI KHAMA PA ULALIKI
Ulendo Woyamba: (Mph. 2 kapena zocepelapo) wp16 Na. 6 nkhani ya pacikuto—Gaŵilani khadi yongenela pa webusaiti yathu.
Ulendo Wobwelelako: (Mph. 4 kapena zocepelapo) wp16. Na. 6 nkhani ya pacikuto—Welengani lemba pa foni kapena pa tabuleti.
Phunzilo la Baibo: (Mph. 6 kapena zocepelapo) bh tsa. 22-23 ndime 11-12—Itanilani wophunzilayo ku misonkhano.
UMOYO WATHU WACIKHIRISTU
“Mmene Tingaseŵenzetsele Buku la Zimene Baibulo Ingatiphunzitse”: (Mph. 15) Kukambilana. Pambuyo pake, tambitsani ndi kukambilana vidiyo yoonetsa wofalitsa acititsa phunzilo la Baibo mwa kuseŵenzetsa Mfundo 4 pa tsamba 115 m’buku la Zimene Baibulo Ingatiphunzitse. Ngati vidiyo palibe, citani citsanzo coonetsa mmene tingacititsile phunzilo mwa kuseŵenzetsa Mfundo 4 pa tsamba 115 m’buku la Zimene Baibulo Ingatiphunzitse.
Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) kr nkhani 4 ndime 1-6, ndi bokosi pa tsa. 43”
Kubwelelamo na Kuchulako za Mlungu Wotsatila (Mph. 3)
Nyimbo 112 na Pemphelo