Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU | MLALIKI 1–6

Muzikondwela Pogwila Nchito Mwakhama

Muzikondwela Pogwila Nchito Mwakhama

Yehova amafuna kuti tizikondwela na nchito yathu, ndipo amatiuza zimene zingatithandize. Munthu angayambe kukondwela na nchito yake ngati amaiona moyenela.

Kuti muzikondwela na nchito yanu, mufunika . . .

3:13; 4:6

  • kukhala na maganizo oyenela

  • kuganizila mmene nchito yanu imapindulitsila ena

  • kugwila nchito mwakhama. Koma mukakomboka, muzikhala na nthawi yoceza na banja lanu ndi kucita zinthu zauzimu