Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

November 21-27

MLALIKI 7-12

November 21-27
  • Nyimbo 41 na Pemphelo

  • Mau Oyamba (Mph. 3 kapena zocepelapo)

CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU

  • Kumbukila Mlengi Wako Wamkulu Masiku a Unyamata Wako”: (Mph. 10)

    • Mlal. 12:1—Acicepele angaseŵenzetse nthawi na mphamvu zawo potumikila Mulungu (w14 1/1, tsa. 18 ndime 3; tsa. 22 ndime 1)

    • Mlal. 12:2-7—Acicepele angacite zambili “asanafike masiku oipa” amene amabwela cifukwa ca ukalamba (w08 11/15-CN, tsa. 23 ndime 2; w06 11/1-CN, tsa. 16 ndime 9)

    • Mlal. 12:13, 14—Kutumikila Yehova kungakuthandizeni kukhala na umoyo wabwino kwambili (w11 11/1-CN, tsa. 21 ndime 1-6)

  • Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (Mph. 8)

    • Mlal. 10:1—Zingatheke bwanji kuti ‘ucitsilu pang’ono uwononge mbili ya munthu amene akulemekezedwa cifukwa ca nzelu’? (w06 11/1-CN, tsa. 16 ndime 5)

    • Mlal. 11:1—Kodi mau akuti “tumiza mkate wako pamadzi” atanthauza ciani? (w06 11/1-CN, tsa. 16 ndime 7)

    • Kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno kwaniphunzitsa ciani za Yehova?

    • Ni mfundo ziti pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno zimene ningaseŵenzetse mu ulaliki?

  • Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4 kapena zocepelapo) Mlal. 10:12–11:10

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Ulendo Woyamba: (Mph. 2 kapena zocepelapo) 2 Tim. 3:1-5—Phunzitsani Coonadi.

  • Ulendo Wobwelelako: (Mph. 4 kapena zocepelapo) Yes. 44:27–45:2—Phunzitsani Coonadi.

  • Phunzilo la Baibo: (Mph. 6 kapena zocepelapo) bh masa. 25-26 ndime 18-20

UMOYO WATHU WACIKHIRISTU