Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU MLALIKI 7–12

“Kumbukila Mlengi Wako Wamkulu Masiku a Unyamata Wako”

“Kumbukila Mlengi Wako Wamkulu Masiku a Unyamata Wako”

Kumbukilani Mlengi wanu Wamkulu mukali acicepele mwa kuseŵenzetsa maluso anu pom’tumikila

12:1, 13

  • Acicepele ambili ali ndi thanzi ndi mphamvu cakuti angakwanitse kugwila nchito zovuta

  • Acicepele ayenela kuseŵenzetsa nthawi na mphamvu zawo potumikila Yehova pamene akalibe kufooka na ukalamba

Solomo anafotokoza mavuto a ukalamba mwandakatulo

12:2-7

  • Vesi 3: “Akazi oyang’ana pawindo azidzaona mdima”

    Kusayang’ana bwino

  • Vesi 4: “Ana onse aakazi azidzaimba nyimbo ndi mau otsika”

    Kuvutika kumva

  • Vesi 5: “Zakudya sizidzakoma”

    Kusamvela kukoma kwa cakudya