November 28–December 4
NYIMBO YA SOLOMO 1-8
Nyimbo 106 na Pemphelo
Mau Oyamba (Mph. 3 kapena zocepelapo)
CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU
“Mtsikana Wacisulami n’Citsanzo Cabwino Cofunika Kutengela”: (Mph. 10).)
[Tambitsani vidiyo yakuti Mfundo Zokhudza Buku la Nyimbo ya Solomo.]
Nyimbo 2:7; 3:5—Msulami anayesetsa kuyembekezela mwamuna amene akanamukonda na mtima wonse (w15 1/15 tsa. 31 ndime 11-13)
Nyimbo 4:12; 8:8-10—Pamene anali kuyembekezela, anakhalabe wokhulupilika ndi wodziletsa (w15 1/15 tsa. 32 ndime 14-16)
Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (Mph. 8)
Nyimbo 2:1—Ni makhalidwe ati amene anapangitsa Msulami kukhala wokongola kwambili? (w15 1/15 tsa. 31 ndime 13)
Nyimbo 8:6—N’cifukwa ciani Baibo imakamba kuti cikondi ceni-ceni ni “lawi la Ya”? (w15 1/15 tsa. 29 ndime 3; w06 11/15-CN, tsa. 20 ndime 7)
Kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno kwaniphunzitsa ciani za Yehova?
Ni mfundo ziti pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno zimene ningaseŵenzetse mu ulaliki?
Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4 kapena zocepelapo) Nyimbo 2:1-17
CITANI KHAMA PA ULALIKI
Ulendo Woyamba: (Mph. 2 kapena zocepelapo) bh—Seŵenzetsani vidiyo yakuti N’cifukwa ciani muyenela kuphunzila Baibulo? pofotokoza mmene timaphunzilila bukuli. (Cidziŵitso: Musatambitsedi vidiyo imeneyi pocita citsanzo koma mungoyelekezela cabe)
Ulendo Wobwelelako: (Mph. 4 kapena zocepelapo) bh—Itanilani munthuyo ku misonkhano.
Phunzilo la Baibo: (Mph. 6 kapena zocepelapo) bh masa. 29-31 ndime 8-9
UMOYO WATHU WACIKHIRISTU
“Kodi Ndafika Poti N’kukhala ndi Chibwenzi?”: (Mph. 9) Nkhani yozikidwa pa nkhani yakuti “Kodi Ndafika Poti N’kukhala ndi Chibwenzi” (Pitani pa webusaiti ya m’Chichewa ndi kuona pa ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZITSA > ACINYAMATA.)
Ndi Cikondi Ceni-ceni Kapena Kutengeka Maganizo Cabe?: (Mph. 6) Tambitsani na kukambilana vidiyo ya tukadoli yakuti Ndi Cikondi Ceni-Ceni Kapena Kutengeka Maganizo Cabe? (Pitani pa Videos ndi kuona mbali yakuti OUR MEETINGS AND MINISTRY) Ngati vidiyo palibe, kambilanani nkhani pa tsamba 205 ndi 206 m’buku la Zimene Achinyamata Amafunsa buku laciwili.
Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) kr nkhani 4 ndime 16-23 na bokosi pa tsa. 48
Kubwelelamo na Kuchulako za Mlungu Wotsatila (Mph. 3)
Nyimbo 34 na Pemphelo