Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU | NYIMBO YA SOLOMO 1-8

Mtsikana Wacisulami n’Citsanzo Cabwino Cofunika Kutengela

Mtsikana Wacisulami n’Citsanzo Cabwino Cofunika Kutengela

N’ciani cinam’pangitsa kukhala citsanzo cabwino kwa alambili a Yehova?

2:7; 4:12

  • Anayembekezela mwamuna amene akanamukondadi

  • Anakana kuti ena amusonkhezele kukhala pa cisumbali na munthu aliyense amene anamufunsila

  • Anali wodzicepetsa, wofatsa, ndi wodziletsa

  • Sananyengeke na golide kapena mau okopa

Dzifunseni kuti:

‘Ni khalidwe liti la mtsikana wa cisulami limene niyenela kutengela?’