Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

Makambilano Acitsanzo

Makambilano Acitsanzo

●○○ ULENDO WOYAMBA

Funso: Kodi colinga ca moyo n’ciani?

Lemba: Gen. 1:27, 28

Ulalo: N’cifukwa ciani tingakhale otsimikiza kuti Mulungu adzakwanilitsa colinga cake?

○●○ ULENDO WOBWELELAKO WOYAMBA

Funso: N’cifukwa ciani tingakhale otsimikiza kuti Mulungu adzakwanilitsa colinga cake?

Lemba: Yos. 21:45

Ulalo: Kodi Mulungu watilonjeza ciani kutsogolo?

○○● ULENDO WOBWELELAKO WACIŴILI

Funso: Kodi Mulungu watilonjeza ciani kutsogolo?

Lemba: Chiv. 21:4

Ulalo: Tingacite ciani kuti tikalandile madalitso amene Mulungu anatilonjeza?