Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

November 18-24

CHIVUMBULUTSO 1-3

November 18-24
  • Nyimbo 15 na Pemphelo

  • Mawu Oyamba (3 min. olo kucepelapo)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • Ndikudziŵa Nchito Zako”: (10 min.)

    • [Tambitsani vidiyo yakuti Mfundo Zokhudza Buku la Chivumbulutso.]

    • Chiv. 1:20—Yesu amadziŵa ciliconse cokhudza akulu mu mpingo (w12 10/15 14 ¶8)

    • Chiv. 2:1, 2—Yesu adziŵa zimene zikucitika mu mpingo uliwonse (w12 4/15 29 ¶11; w01 1/15 20-21 ¶20)

  • Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (8 min.)

    • Chiv. 1:7—Kodi diso lililonse lidzamuona bwanji Yesu pamene “akubwela ndi mitambo”? Nanga zimenezi zidzacitika liti? (kr 226 ¶8, 10)

    • Chiv. 2:7—Kodi kudya za “mumtengo wa moyo . . .m’paradaiso wa Mulungu” kumatanthauza ciani? (w09 1/15 31 ¶1)

    • Kodi imwe pacanu, kuŵelenga Baibo kwa wiki ino kwakuphunzitsani ciani za Yehova?

    • Ni cuma ca kuuzimu cina citi cimene mwapeza pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino?

  • Kuŵelenga Baibo: (4 min. olo kucepelapo) Chiv. 1:1-11 (th phunzilo 5)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

UMOYO WATHU WACIKHRISTU