Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

November 4-10

1 YOHANE 1-5

November 4-10
  • Nyimbo 122 na Pemphelo

  • Mawu Oyamba (3 min. olo kucepelapo)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • Musamakonde Dziko Kapena Zinthu za M’dziko”: (10 min.)

    • [Tambitsani vidiyo yakuti Mfundo Zokhudza Buku la 1 Yohane.]

    • 1 Yoh. 2:15, 16—‘Ciliconse ca m’dziko . .  sicicokela kwa Atate, koma kudziko’ (w05 1/1 10 ¶13)

    • 1 Yoh. 2:17—Dziko likupita limodzi na cilako-lako cake (w13 8/1 27 ¶18)

  • Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (8 min.)

    • 1 Yoh. 2:7, 8—Kodi lamulo limene Yohane anakamba pa mavesiwa linakhala bwanji lakale ndiponso latsopano? (w13 9/1 10 ¶14)

    • 1 Yoh. 5:16, 17—Kodi chimo “lobweletsa imfa” n’lotani? (it-1 862 ¶5)

    • Kodi imwe pacanu, kuŵelenga Baibo kwa wiki ino kwakuphunzitsani ciani za Yehova?

    • Ni cuma ca kuuzimu cina citi cimene mwapeza pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino?

  • Kuŵelenga Baibo: (4 min. olo kucepelapo) 1 Yoh. 1:1–2:6 (th phunzilo 5)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Citani Khama pa Kuŵelenga na Kuphunzitsa: (10 min.) Kukambilana. Tambitsani vidiyo yakuti Kukamba Mwaumoyo. Ndiyeno, kambilanani phunzilo 11 m’bulosha ya Kuphunzitsa.

  • Nkhani: (5 min. olo kucepelapo) w04 10/1 29—Mutu: Kodi Yohane anatanthauzanji pa 1 Yohane 4:18, pamene anakamba kuti “cikondi cimene cili cokwanila cimathetsa mantha”? (th phunzilo 7)

UMOYO WATHU WACIKHRISTU