1 YOHANE 1-5
CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU |Musamakonde Dziko Kapena Zinthu za M’dziko
2:15-17
Satana amaseŵenzetsa zinthu zitatu zotsatilazi, zimene ni zokopa za dzikoli, pofuna kuticotsa kwa Yehova. Kodi zinthu zimenezi mungazifotokoze bwanji kwa munthu wina?
-
“Cilakolako ca thupi”
-
“Cilakolako ca maso”
-
“Kudzionetsela ndi zimene munthu ali nazo pa moyo wake”