Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

November 23-29

LEVITIKO 6-7

November 23-29
  •  Nyimbo 46 na Pemphelo

  •  Mawu Oyamba (1 min.)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • Njila Yoonetsela Kuyamikila”: (10 min.)

    • Lev. 7:11, 12—Nsembe zina zaciyanjano zinali kupelekedwa monga nsembe yaufulu yoonetsa ciyamikilo kwa Yehova (w19.11 22 ¶9)

    • Lev. 7:13-15—Munthu akapeleka nsembe yaciyanjano pamodzi na banja lake, zinali monga kuti akudyela pamodzi na Yehova, kuonetsa kuti ali naye pa ubale wabwino (w00 8/15 15 ¶15)

    • Lev. 7:20—Nsembe yaciyanjano inali kukhala yovomelezeka kokha ngati wopelekayo anali woyela (w00 8/15 19 ¶8)

  • Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (10 min.)

    • Lev. 6:13—Kodi Ayuda amakhulupilila kuti moto wa paguwa unayamba bwanji? Koma kodi n’ciani cimene Malemba amaonetsa? (it-1 833 ¶1)

    • Lev. 6:25—Kodi nsembe zamacimo zinali kusiyana bwanji na nsembe zopseleza komanso zaciyanjano? (si 27 ¶15)

    • Pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino, ni mfundo yopindulitsa iti imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?

  • Kuŵelenga Baibo: (4 min. olo kucepelapo) Lev. 6:1-18 (th phunzilo 5)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 18

  • Khala Bwenzi la Yehova—Khalani Woyamikila: (5 min.) Tambitsani vidiyo imeneyi. Ndiyeno itanilani ku pulatifomu ana angapo amene munawakonzekeletsa, ngati alipo, na kuwafunsa mafunso okhudzana na vidiyo imene atamba.

  • Zofunikila za Mpingo: (10 min.)

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min. olo kucepelapo) lfb phunzilo 3, 4

  • Mawu Othela (3 min. olo kucepelapo)

  • Nyimbo 31 na Pemphelo