LEVITIKO 6–7
CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU |Njila Yoonetsela Kuyamikila
7:11-15, 20
Nsembe zaciyanjano zimene Aisiraeli anali kupeleka zimatikumbutsa kufunika koyamikila Yehova m’mapemphelo athu komanso mwa khalidwe lathu.—Afil. 4:6, 7; Akol. 3:15.
-
Popemphela, kodi tingamuyamikile Yehova pa zinthu ziti?—1 Ates. 5:17, 18
-
Kodi kuonetsa kuyamikila kumatipindulitsa bwanji?
-
Kodi zingatheke bwanji munthu kudya “pathebulo la ziwanda”? Nanga kucita zimenezi kungaonetse bwanji kuti sitiyamikila kwa Yehova?—1 Akor. 10:20, 21