December 6-12
OWERUZA 6–7
Nyimbo 38 na Pemphelo
Mawu Oyamba (Mph. 1)
CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Pita ndi Mphamvu Zimene Ndakupatsazi”: (Mph. 10)
Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)
Ower. 6:27—Kodi citsanzo ca Gidiyoni cingatithandize bwanji mu ulaliki? (w05 1/15 26 ¶6)
Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo yopindulitsa iti imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?
Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) Ower. 6:1-16 (th phunzilo 10)
CITANI KHAMA PA ULALIKI
Vidiyo ya Ulendo Woyamba: (Mph. 5) Kukambilana. Onetsani vidiyo yakuti Ulendo Woyamba: Baibo—Aroma 15:4. Nthawi iliyonse vidiyo ikaima, na imwe iimitseni na kufunsa omvetsela mafunso amene aonekela mu vidiyo.
Ulendo Woyamba: (Mph. 4) Yambani na makambilano acitsanzo. Ndiyeno gaŵilani kabuku kakuti Kondwelani na Moyo Kwamuyaya! (th phunzilo 6)
Ulendo Woyamba: (Mph. 4) Yambani na makambilano acitsanzo. Ndiyeno gaŵilani kabuku kakuti Kondwelani na Moyo Kwamuyaya! na kuonetsa mwininyumba mmene angacitile daunilodi kabuku ka pa cipangizo. (th phunzilo 15)
UMOYO WATHU WACIKHRISTU
“Nchito Yovuta Kwambili Inatheka Cifukwa ca Mzimu Woyela”: (Mph. 15) Kukambilana. Onetsani vidiyo yakuti Kupanga ‘Vidiyo Yakuti “The New World Society in Action”
Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) lfb phunzilo 67
Mawu Othela (Mph. 3)
Nyimbo 55 na Pemphelo