December 19-25
2 MAFUMU 18-19
Nyimbo 148 na Pemphelo
Mawu Oyamba (Mph. 1)
CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Zimene Adani Athu Amacita Poyesa Kutifooketsa”: (Mph. 10)
Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)
2 Maf. 19:37—Kodi vesiyi ionetsa bwanji kufunika kounika mosamala maumboni a zinthu zofukulidwa m’matongwe? (it-1 155 ¶4)
Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo yopindulila iti imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?
Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) 2 Maf. 18:1-12 (th phunzilo 5)
CITANI KHAMA PA ULALIKI
Ulendo Woyamba: (Mph. 3) Makambilano anu atsamile pa mfundo yaikulu ya makambilano acitsanzo. Itanilani munthuyo ku misonkhano. Chulani na kukambilanako za mu vidiyo yakuti N’ciani Cimacitika ku Nyumba ya Ufumu? (Koma musaitambitse) (th phunzilo 1)
Ulendo Wobwelelako: (Mph. 4) Makambilano anu atsamile pa mfundo yaikulu ya makambilano acitsanzo. M’fotokozeleni mmene phunzilo la Baibo limacitikila na kum’patsa kakhadi kofunsila phunzilo la Baibo. (th phunzilo 2)
Nkhani: (Mph. 5) w20.11 15 ¶14—Mutu: Muzipemphelela Amene Akuzunzidwa —Motani? (th phunzilo 14)
UMOYO WATHU WACIKHRISTU
“Kondwelani Pamene Mukuzunzidwa”: (Mph. 8) Kukambilana. Onetsani vidiyo yakuti Tingakhalebe Okondwela Ngakhale pa Mazunzo.
Zofunikila za Mpingo: (Mph. 7)
Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) lff phunzilo 32 mfundo 1-4, komanso chati yakuti “Mmene Maloto a Mtengowo Akukhudzila Ufumu wa Mulungu”
Mawu Othela (Mph. 3)
Nyimbo 22 na Pemphelo