Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

November 21-27

2 MAFUMU 9-10

November 21-27

Nyimbo 126 na Pemphelo

Mawu Oyamba (Mph. 1)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Anacita Zinthu Molimba Mtima, Modzipeleka, Komanso Mokangalika”: (Mph. 10)

Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)

2 Maf. 10:29, 31—Kodi tiphunzilapo ciyani pa colakwa ca Yehu? (w11 11/15 5 ¶6-7)

Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo yopindulila iti imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?

Kuŵelenga Baibo:

(Mph. 4) 2 Maf. 9:1-14 (th phunzilo 10)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

Ulendo Woyamba: (Mph. 3) Makambilano anu atsamile pa mfundo yaikulu ya makambilano acitsanzo. Mugaŵileni cofalitsa ca mu Thuboksi yathu. (th phunzilo 1)

Ulendo Wobwelelako: (Mph. 4) Makambilano anu atsamile pa mfundo yaikulu ya makambilano acitsanzo. M’fotokozeleni mmene phunzilo la Baibo laulele limacitikila, na kum’gaŵila kabuku kakuti Kondwelani na Moyo Kwamuyaya! Chulani na kukambilanako za vidiyo yakuti Kodi Phunzilo la Baibulo Limacitika Bwanji? (Koma musaitambitse.) (th phunzilo 12)

Nkhani: (Mph. 5) w13 5/15 8-9 ¶3-6—Mutu: Tengelani Yehova na Yesu pa Nkhani ya Kudzipeleka. (th phunzilo 16)

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

Nyimbo 64

Zimene Anzanu Amakamba—Kuzengeleza: (Mph. 5) Kukambilana. Onetsani vidiyoyi. Ndiyeno funsani omvela mafunso awa: N’zinthu ziti zingapangitse munthu kuzengeleza? N’cifukwa ciyani timakhala acimwemwe ngati sitizengeleza pocita zinthu?

Zimene Zingakuthandizeni Kupewa Kuzengeleza”: (Mph. 10) Kukambilana.

Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) lff phunzilo 28

Mawu Othela (Mph. 3)

Nyimbo 19 na Pemphelo