December 11-17
YOBU 25-27
Nyimbo 34 na Pemphelo
Mawu Oyamba (Mph. 1)
CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Tingakhale na Mtima Wosagaŵikana Ngakhale Ndife Opanda Ungwilo”: (Mph. 10)
Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)
Yobu 26:14—Kodi zocepa zimene timadziŵako za cilengedwe zimatithandiza kudziŵa ciyani zokhudza Yehova? (w16.11 9 ¶3)
Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo iti yokupindulilani imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?
Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) Yobu 25:1–26:14 (th phunzilo 12)
CITANI KHAMA PA ULALIKI
Ulendo Woyamba: (Mph. 2) Makambilano anu atsamile pa mfundo yaikulu ya makambilano acitsanzo. Mukayamba, mwininyumba akambe mawu ofala kwanuko ofuna kukanila ulaliki. Koma mwaluso loŵelani pa mawu amenewo. (th phunzilo 1)
Ulendo Wobwelelako: (Mph. 5) Makambilano anu atsamile pa mfundo yaikulu ya makambilano acitsanzo. Onetsani munthuyo mmene angapezele nkhani imene yamucititsa cidwi pa jw.org. (th phunzilo 17)
Phunzilo la Baibo: (Mph. 5) lff phunzilo 13 mawu oyamba na mfundo 1-3 (th phunzilo 15)
UMOYO WATHU WACIKHRISTU
“Kugwilizana Pakati pa Kusunga Umphumphu na Maganizo Athu”: (Mph. 5) Kukambilana.
Zimene Gulu Lakwanitsa Kucita: (Mph. 10) Onetsani vidiyo yakuti Zimene Gulu Lakwanitsa Kucita ya December.
Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) bt mutu 3 ¶4-11
Mawu Othela (Mph. 3)
Nyimbo 57 na Pemphelo