December 25-31
YOBU 30-31
Nyimbo 28 na Pemphelo
Mawu Oyamba (Mph. 1)
CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Zimene Zinathandiza Yobu Kukhalabe Woyela”: (Mph. 10)
Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)
Yobu 31:35—Kodi tingapewe bwanji kukhala monga anzake a Yobu ngati wina watiuzako mavuto ake? (w05 11/15 11 ¶3)
Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo iti yokupindulilani imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?
Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) Yobu 31:15-40 (th phunzilo 5)
CITANI KHAMA PA ULALIKI
Ulendo Woyamba: (Mph. 4) Makambilano anu atsamile pa mfundo yaikulu ya makambilano acitsanzo. Muuzeni za pulogilamu yathu yophunzitsa Baibo, na kum’patsa kakhadi kopemphela phunzilo la Baibo. (th phunzilo 1)
Ulendo Wobwelelako: (Mph. 3) Makambilano anu atsamile pa mfundo yaikulu ya makambilano acitsanzo. Itanilani munthuyo ku misonkhano. Chulani na kukambilanako vidiyo yakuti N’ciani Cimacitika ku Nyumba ya Ufumu? (Koma musaitambitse) (th phunzilo 11)
Nkhani: (Mph. 5) g16.4 8-9—Mutu: Kodi Ningafotokoze Bwanji Zimene Baibo Imakamba pa Nkhani ya Mathanyula? (th phunzilo 14)
UMOYO WATHU WACIKHRISTU
“Cifukwa Cake Kuonelela Zamalisece N’koipa”: (Mph. 7) Kukambilana na kutamba vidiyo.
Zofunikila za Mpingo: (Mph. 8)
Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) bt mutu 4 ¶1-8
Mawu Othela (Mph. 3)
Nyimbo 74 na Pemphelo