Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Zimene Zinathandiza Yobu Kukhalabe Woyela

Zimene Zinathandiza Yobu Kukhalabe Woyela

Yobu anacita pangano na maso ake (Yobu 31:1; w10 4/15 21 ¶8)

Yobu anaganizila zotulukapo za kucita coipa (Yobu 31:​2, 3; w08 9/1 11 ¶4)

Iye anali kukumbukila kuti Yehova amaona khalidwe lake (Yobu 31:4; w10 11/15 5-6 ¶15-16)

Kukhala woyela kumatanthauza kukhala waukhondo ndiponso wosaipitsidwa, osati kunja kokha koma na mkati momwe. Timafuna kukhala woyela na mumtima momwe.—Mat. 5:28.