November 6-12
YOBU 13-14
Nyimbo 151 na Pemphelo
Mawu Oyamba (Mph. 1)
CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Munthu Akafa, Kodi Angakhalenso Ndi Moyo?”: (Mph. 10)
Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)
Yobu 13:12—N’cifukwa ciyani Yobu anayelekezela zokamba za anzake acinyengo na “miyambi yopanda pake ngati phulusa”? (it-1 191)
Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo iti yokupindulilani imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?
Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) Yobu 13:1-28 (th phunzilo 12)
CITANI KHAMA PA ULALIKI
Vidiyo ya Ulendo Woyamba: (Mph. 5) Kukambilana. Tambitsani vidiyo yakuti Ulendo Woyamba: Baibo—2 Tim. 3:16, 17. Nthawi zonse vidiyo ikaima, inunso iimitseni na kufunsa omvela mafunso amene aonekela.
Ulendo Woyamba: (Mph. 3) Makambilano anu atsamile pa mfundo yaikulu ya makambilano acitsanzo. Kenako m’gaŵileni bulosha yakuti Kondwelani na Moyo Kwamuyaya! (th phunzilo 2)
Phunzilo la Baibo: (Mph. 5) lff mafunso obweleza a cigawo 1, mafunso 1-5 (th phunzilo 19)
UMOYO WATHU WACIKHRISTU
“‘Muziika Kenakake Pambali’”: (Mph. 15) Kukambilana na kutamba vidiyo. Ikambidwe na mkulu. Yamikilani mpingo cifukwa copeleka ndalama zimene zimathandiza kupititsa patsogolo zinthu za Ufumu.
Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) bt mutu 1 ¶16-21
Mawu Othela (Mph. 3)
Nyimbo 76 na Pemphelo