November 11-17
SALIMO 106
Nyimbo 36 na Pemphelo | Mawu Oyamba (Mph. 1)
1. “Iwo Anaiwala Mulungu, Mpulumutsi Wawo”
(Mph. 10)
Aisiraeli atacita mantha, anapandukila Yehova (Eks. 14:11, 12; Sal. 106:7-9)
Pamene Aisiraeli anali na njala komanso ludzu, anayamba kung’ung’udzila Yehova (Eks. 15:24; 16:3, 8; 17:2, 3; Sal. 106:13, 14)
Iwo atada nkhawa, anayamba kulambila mafano (Eks 32:1; Sal 106:19-21; w18.07 20 ¶13)
ZOFUNIKA KUZISINKHASINKHA: Tikakumana na zovuta, kodi timapindula bwanji tikakumbukila mmene Yehova anatithandizilapo m’mbuyomu?
2. Kufufuza Cuma Cauzimu
(Mph. 10)
Sal. 106:36, 37—Kodi pali kugwilizana kotani pakati pa kulambila mafano na nsembe zopelekedwa ku ziŵanda? (w06-CN 7/15 13 ¶9)
Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, munapeza mfundo zothandiza ziti zimene mungakonde kutifotokozelako?
3. Kuŵelenga Baibo
(Mph. 4) Sal. 106:21-48 (th phunzilo 10)
4. Kuphunzitsa M’njila Yosavuta Kumva—Mmene Yesu Anacitila Zimenezi
(Mph. 7) Kukambilana. Tambitsani VIDIYO, kenako kambilanani lmd phunzilo 11 mfundo 1-2.
5. Kuphunzitsa M’njila Yosavuta Kumva—Tengelani Citsanzo ca Yesu
(Mph. 8) Kukambilana. Seŵenzetsani lmd phunzilo 11 mfundo 3-5 komanso mbali yakuti “Onaninso Malemba Awa.”
Nyimbo 78
6. Zofunikila za Mpingo
(Mph. 15)
7. Phunzilo la Baibo la Mpingo
(Mph. 30) bt mutu 18 ¶1-5, bokosi pa mas. 142, 144