December 2-8
MASALIMO 113-118
Nyimbo 127 na Pemphelo | Mawu Oyamba (Mph. 1)
1. Kodi Tidzamubwezela Ciyani Yehova?
(Mph. 10)
Yehova amatiteteza, amacita nafe zinthu mokoma mtima komanso amatipulumutsa (Sal. 116:6-8; w01-CN 1/1 11 ¶13)
Tingamubwezele zabwino Yehova mwa kutsatila malamulo na mfundo zake pa umoyo wathu wonse (Sal. 116:12, 14; w09-CN 7/15 29 ¶4-5)
Tingamubwezele zabwino Yehova mwa kupeleka ‘nsembe zomuyamikila’ (Sal. 116:17; w19.11 22-23 ¶9-11)
2. Kufufuza Cuma Cauzimu
(Mph. 10)
Sal. 116:15—Kodi anthu a Mulungu “okhulupilika” ochulidwa pa vesili ndani? (w12-CN 5/15 22 ¶1-2)
Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, munapeza mfundo zothandiza ziti zimene mungakonde kutifotokozelako?
3. Kuŵelenga Baibo
(Mph. 4) Sal. 116:1–117:2 (th phunzilo 2)
4. Kulimba Mtima—Mmene Yesu Anaonetsela Khalidwe Limeneli
(Mph. 7) Kukambilana. Tambitsani VIDIYO, kenako kambilanani lmd phunzilo 12 mfundo 1-2.
5. Kulimba Mtima—Tengelani Citsanzo ca Yesu
(Mph. 8) Kukambilana. Seŵenzetsani lmd phunzilo 12 mfundo 3-5 komanso mbali yakuti “Onaninso Malemba Awa”
Nyimbo 60
6. Zofunikila za Mpingo
(Mph. 15)
7. Phunzilo la Baibo la Mpingo
(Mph. 30) bt mutu 19 ¶1-5, mabokosi pa mas. 149-150