Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

October 24-30

MIYAMBO 17-21

October 24-30
  • Nyimbo 76 na Pemphelo

  • Mau Oyamba (Mph. 3 kapena zocepelapo)

CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU

  • Muziyesetsa Kukhala Mwamtendele na Ena”: (Mph. 10)

    • Miy. 19:11—Muzikhala wodekha wina akakukhumudwitsani (w14 12/1-CN, masa. 12-13)

    • Miy. 18:13, 17; 21:13—Onetsetsani kuti mwamvetsetsa nkhani yonse (w11 8/15-CN, tsa. 30 ndime 11-14)

    • Miy. 17:9—Muzikhululukila amene akulakwilani (w11 8/15-CN, tsa. 31 ndime 17)

  • Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (Mph. 8)

    • Miy. 17:5—Chulani cifukwa cimodzi cimene tifunika kusankhila zosangulutsa mwanzelu. (w10 11/15-CN, tsa. 6 ndime 17; w10 11/15-CN, tsa. 31 ndime 15)

    • Miy. 20:25—Kodi mfundo imeneyi igwila nchito bwanji ngati munthu ali pa cisumbali kapena m’cikwati? (w09 5/15-CN, masa. 15-16 ndime 12-13)

    • Kuŵelenga Baibulo kwa mlungu uno kwaniphunzitsa ciani za Yehova?

    • Ni mfundo ziti pa kuŵelenga Baibulo kwa mlungu uno zimene ningaseŵenzetse mu ulaliki?

  • Kuŵelenga Baibulo: (Mph. 4 kapena zocepelapo) Miy. 18:14–19:10

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Ulendo Woyamba: (Mph. 2 kapena zocepelapo) Gaŵilani kapepa koitanila anthu ku misonkhano. (inv)

  • Ulendo Wobwelelako: (Mph. 4 kapena zocepelapo) inv—Tsilizani na mau oonetsa kuti mufuna kumutambitsa vidiyo yakuti N’ciani Cimacitika ku Nyumba ya Ufumu?

  • Phunzilo la Baibulo: (Mph. 6 kapena zocepelapo) lv tsa. 57 ndime 14-15—Thandizani wophunzila kuona kuti afunika kuvala na kudzikonza moyenela popita kumisonkhano.

UMOYO WATHU WACIKHIRISTU