October 1-7
YOHANE 9-10
Nyimbo 25 na Pemphelo
Mawu Oyamba (3 min. olo kucepelapo)
CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Yesu Amasamalila Nkhosa Zake”: (10 min.)
Yoh. 10:1-3, 11, 14—Yesu, amene ni “m’busa wabwino,” amazidziŵa nkhosa zake ndipo amasamalila zosoŵa zawo mokwanila (“Khola la Nkhosa” nwtsty zithunzi; w11 5/15 mape. 7-8 pala. 5)
Yoh. 10:4, 5—Nkhosa zimadziŵa mawu a Yesu, osati a alendo (cf mape. 124-125 pala. 17)
Yoh. 10:16—Nkhosa za Yesu zimakhala mogwilizana (“kuzitenga” nwtsty mfundo younikila)
Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (8 min.)
Yoh 9:38—N’cifukwa ciani wopempha-pempha wakhungu anagwadila Yesu? (“anam’gwadila iye” nwtsty mfundo younikila)
Yoh. 10:22—N’cifukwa ciani Ayuda anali kucita Cikondwelelo ca Kupeleka Kacisi kwa Mulungu? (“Cikondwelelo ca Kupeleka Kacisi” nwtsty mfundo younikila)
Kodi kuŵelenga Baibo kwa wiki ino kwakuphunzitsani ciani za Yehova?
Ni cuma ca kuuzimu cina citi cimene mwapeza pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino?
Kuŵelenga Baibo: (4 min. olo kucepelapo) Yoh. 9:1-17
CITANI KHAMA PA ULALIKI
Vidiyo ya Ulendo Woyamba: (4 min.) Tambitsani na kukambilana vidiyoyi.
Kubwelelako Koyamba: (3 min. olo kucepelapo) Seŵenzetsani makambilano acitsanzo.
Phunzilo la Baibo: (6 min. olo kucepelapo) fg phunzilo 14 mapa. 1-2