Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

October 22-28

Yohane 15-17

October 22-28
  • Nyimbo 129 na Pemphelo

  • Mawu Oyamba (3 min. olo kucepelapo)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • Simuli Mbali ya Dzikoli”: (10 min.)

    • Yoh. 15:19—Otsatila a Yesu sali “mbali ya dzikoli” (“dzikolinwtsty mfundo younikila)

    • Yoh. 15:21—Otsatila a Yesu amazondewa cifukwa ca dzina lake (“cifukwa ca dzina langanwtsty mfundo younikila)

    • Yoh. 16:33—Otsatila a Yesu angagonjetse dziko ngati atengela citsanzo cake (it-1 peji 516)

  • Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (8 min.)

    • Yoh. 17:21-23—Kodi ophunzila a Yesu anali kudzakhala “amodzi” m’lingalilo lotani? (“amodzi” “akhale mu umodzi weni-weninwtsty mfundo zounikila)

    • Yoh. 17:24—Kodi “maziko a dziko” n’ciani? (“maziko a dzikonwtsty mfundo younikila)

    • Kodi imwe pacanu, kuŵelenga Baibo kwa wiki ino kwakuphunzitsani ciani za Yehova?

    • Ni cuma ca kuuzimu cina citi cimene mwapeza pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino?

  • Kuŵelenga Baibo: (4 min. olo kucepelapo) Yoh. 17:1-14

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Kubwelelako Kaciŵili: (3 min. olo kucepelapo) Seŵenzetsani makambilano acitsanzo.

  • Kubwelelako Kacitatu: (3 min. olo kucepelapo) Sankhani mwekha lemba, ndipo gaŵilani cofalitsa cophunzitsila Baibo.

  • Phunzilo la Baibo: (6 min. olo kucepelapo) fg phunzilo 14 mapa. 3-4

UMOYO WATHU WACIKHRISTU