Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

October 29–November 4

Yohane 18-19

October 29–November 4
  • Nyimbo 54 na Pemphelo

  • Mawu Oyamba (3 min. olo kucepelapo)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • Yesu Anacitila Umboni Coonadi”: (10 min.)

    • Yoh. 18:36—Coonadi cimakamba za Ufumu wa Mesiya

    • Yoh. 18:37—Yesu anacitila umboni coonadi cokhudza colinga ca Mulungu (“kudzacitila umboni coonadi,” “coonadinwtsty mfundo zounikila)

    • Yoh. 18:38a—Zioneka kuti Pilato anatsutsa zakuti kuli coonadi (“Coonadi n’ciani?nwtsty mfundo younikila)

  • Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (8 min.)

    • Yoh. 19:30—Kodi mawu akuti Yesu ‘anapeleka mzimu wake’ atanthauza ciani? (“kupeleka mzimu wakenwtsty mfundo younikila)

    • Yoh. 19:31—Kodi pali umboni wabwanji woonetsa kuti Yesu anafa pa Nisani 14, mu 33 C.E.? (“Sabata la tsiku limeneli linali lalikulunwtsty mfundo younikila)

    • Kodi imwe pacanu, kuŵelenga Baibo kwa wiki ino kwakuphunzitsani ciani za Yehova?

    • Ni cuma ca kuuzimu cina citi cimene mwapeza pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino?

  • Kuŵelenga Baibo: (4 min. olo kucepelapo) Yoh. 18:1-14

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Kubwelelako Kaciŵili: (3 min. olo kucepelapo) Yambani na makambilano acitsanzo. Ndiyeno onetsani mwininyumba webusaiti yathu ya jw.org.

  • Kubwelelako Kacitatu: (3 min. olo kucepelapo) Sankhani mwekha lemba na funso lokakambilana ulendo wotsatila.

  • Phunzilo la Baibo: (6 min. olo kucepelapo) fg phunzilo 14 mapa. 6-7

UMOYO WATHU WACIKHRISTU