October 8-14
YOHANE 11-12
Nyimbo 16 na Pemphelo
Mawu Oyamba (3 min. olo kucepelapo)
CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Tengelani Cifundo ca Yesu”: (10 min.)
Yoh. 11:23-26—Yesu anakamba mawu otonthoza kwa Marita (“Ndikudziŵa kuti adzauka” nwtsty mfundo zounikila pa Yoh. 11:24, “Ine ndine kuuka ndi moyo” 25)
Yoh. 11:33-35—Yesu anamva cisoni cacikulu ataona Mariya na anthu ena akulila (“Kulila,” “anadzuma . . . ndi kumva cisoni,” “mu mtima” “kugwetsa misozi” nwtsty mfundo zounikila)
Yoh. 11:43, 44—Yesu anacitapo kanthu kuti athandize anthu
Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (8 min.)
Yoh. 11:49—N’ndani anaika Kayafa kuti akhale mkulu wa ansembe? Nanga anakhala mkulu wa ansembe kwa nthawi yaitali bwanji? (“mkulu wa ansembe” nwtsty mfundo younikila)
Yoh. 12:42—N’cifukwa ciani Ayuda ena anacita mantha kuvomeleza poyela kuti Yesu ni Khristu? (“olamulila,” “angawacotse musunagoge” nwtsty mfundo younikila)
Kodi imwe pacanu, kuŵelenga Baibo kwa wiki ino kwakuphunzitsani ciani za Yehova?
Ni cuma ca kuuzimu cina citi cimene mwapeza pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino?
Kuŵelenga Baibo: (4 min. olo kucepelapo) Yoh. 12:35-50
CITANI KHAMA PA ULALIKI
Ulendo Woyamba: (2 min. olo kucepelapo) Seŵenzetsani makambilano acitsanzo.
Vidiyo ya Kubwelelako Koyamba: (5 min.) Tambitsani na kukambilana vidiyoyi.
Nkhani: (6 min. olo kucepelapo ) w13 9/15 peji 32—Mutu: N’cifukwa Ciani Yesu Anagwetsa Misozi Asanaukitse Lazaro?
UMOYO WATHU WACIKHRISTU
Yesu Ndiye “Kuuka ndi Moyo” (Yoh. 11:25): (15 min.) Kukambilana. Tambitsani vidiyo yakuti ‘Ndithu Mulungu Anamuika Kukhala Ambuye ndi Khristu’—Mbali 2, Kambali Kake. Ndiyeno funsani omvela mafunso otsatilawa: Kodi nkhaniyi itiphunzitsa ciani za cifundo ca Yesu? Kodi Yesu ni “kuuka ndi moyo” m’njila iti? Ni zozizwitsa zotani zimene Yesu adzacita m’tsogolo?
Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min.) jy mutu. 38
Kubwelelamo na Kuchulako za Wiki Yotsatila (3 min.)
Nyimbo 147 na Pemphelo